4 Yehova, muja mudaturuka m'Seiri,Muja mudayenda kucokera ku thengo la Edomu,Dziko linanjenjemera, thambo lomwe linakha,Inde mitambo inakha madzi.
Werengani mutu wathunthu Oweruza 5
Onani Oweruza 5:4 nkhani