18 Musacoke pano, ndikupemphani, mpaka ndikudzerani ndi kuturutsa copereka canga ndi kuciika pamaso panu. Ndipo anati, Ndidzalinda mpaka ubwera.
Werengani mutu wathunthu Oweruza 6
Onani Oweruza 6:18 nkhani