Oweruza 6:19 BL92

19 Ndipo Gideoni analowa, nakonza kambuzi ndi mikate yopanda cotupitsa ya muyeso wa ufa; nyamayi anaiika m'licero, ndi msuzi anauthira mumbale, naturuka nazo kwa iye ali patsinde pa thundu, nazipereka.

Werengani mutu wathunthu Oweruza 6

Onani Oweruza 6:19 nkhani