20 Koma mthenga wa Mulungu ananena naye, Tenga nyamayi ndi mikate yopanda cotupitsa ndi kuziika pathanthwe pano ndi kutsanula msuzi. Ndipo anatero.
Werengani mutu wathunthu Oweruza 6
Onani Oweruza 6:20 nkhani