Oweruza 6:35 BL92

35 Ndipo anatuma mithenga kwa Manase konse; ndi iwonso analalikidwa kumtsata iye; natuma mithenga kwa Aseri, ndi kwa Zebuloni, ndi kwa Nafitali; iwo nadzakomana nao.

Werengani mutu wathunthu Oweruza 6

Onani Oweruza 6:35 nkhani