Oweruza 6:5 BL92

5 Pakuti anakwera nazo zoweta zao ndi mahema ao, analowa ngati dzombe kucuruka kwao; iwowa ndi ngamila zao zomwe nzosawerengeka; ndipo analowa m'dziko kuliononga.

Werengani mutu wathunthu Oweruza 6

Onani Oweruza 6:5 nkhani