Oweruza 6:4 BL92

4 nawamangira misasa, namaononga zipatso za m'dziko mpaka ufika ku Gaza, osawasiyira cocirira njala m'Israyeli, ngakhale nkhosa, kapena ng'ombe, kapena buru.

Werengani mutu wathunthu Oweruza 6

Onani Oweruza 6:4 nkhani