Oweruza 7:1 BL92

1 Pamenepo Yerubaala, ndiye Gideoni, ndi anthu onse okhala naye anauka mamawa, namanga misasa pa citsime ca Harodi, ndi misasa ya Midyani inali kumpoto kwao, pa phiri la More m'cigwa.

Werengani mutu wathunthu Oweruza 7

Onani Oweruza 7:1 nkhani