Oweruza 7:2 BL92

2 Ndipo Yehova anati kwa Gideoni. Anthu ali ndi iwe andicurukira kuti ndipereke Midyani m'dzanja lao; angadzitame Israyeli pa Ine, ndi kuti, Dzanja la ine mwini landipulumutsa.

Werengani mutu wathunthu Oweruza 7

Onani Oweruza 7:2 nkhani