Oweruza 7:3 BL92

3 Ndipo tsopano, kalalike m'makutu a anthu, ndi kuti, Ali yense wocita mantha, nanjenjemera, abwerere nacoke pa phiri la Gileadi. Ndipo anabwererako anthu zikwi makumi awiri mphambu ziwiri, natsalako zikwi khumi.

Werengani mutu wathunthu Oweruza 7

Onani Oweruza 7:3 nkhani