Oweruza 7:15 BL92

15 Ndipo kunali, pakumva Gideoni kufotokozera kwa lotolo ndi tanthauzo lace, anadziwerama; nabwera ku misasa ya Israyeli nati, Taukani, pakuti Yehova wapereka a m'misasa a Midyani m'dzanja lanu.

Werengani mutu wathunthu Oweruza 7

Onani Oweruza 7:15 nkhani