Oweruza 8:1 BL92

1 Ndipo amuna a Efraimu anati kwa iye, Ici waticitira nciani, osatiitana popita iwe kulimbana ndi Amidyani? natsutsana naye kolimba.

Werengani mutu wathunthu Oweruza 8

Onani Oweruza 8:1 nkhani