Oweruza 8:2 BL92

2 Koma ananena nao, Ndacitanji tsopano monga inu? Kodi kukunkha mphesa kwa Efraimu sikuposa kuchera mphesa kwa Abiezeri?

Werengani mutu wathunthu Oweruza 8

Onani Oweruza 8:2 nkhani