Oweruza 8:18 BL92

18 Pamenepo anati kwa Zeba ndi Tsalimuna, Amunawo munawapha ku Tabori anali otani? Iwo nayankha, Monga iwe momwemo iwowa; yense wakunga mwana wa mfumu.

Werengani mutu wathunthu Oweruza 8

Onani Oweruza 8:18 nkhani