20 Nati kwa Yeteri mwana wace woyamba, Tauka, nuwaphe. Koma mnyamatayo sanasolola lupanga lace; pakuti anaopa, pokhala anali mnyamata.
Werengani mutu wathunthu Oweruza 8
Onani Oweruza 8:20 nkhani