22 Pamenepo anthu a Israyeli anati kwa Gideoni, Mutilamulire ndi inu, ndi mwana wanu, ndi mdzukulu wanu, pakuti mwatipulumutsa m'dzanja la Amidyani.
Werengani mutu wathunthu Oweruza 8
Onani Oweruza 8:22 nkhani