28 Motero anagonjetsa Amidyani pamaso pa ana a Israyeli, osaweramutsanso mitu yao iwowa. Ndipo dziko lidapumula zaka makumi anai m'masiku a Gideoni.
Werengani mutu wathunthu Oweruza 8
Onani Oweruza 8:28 nkhani