Oweruza 8:5 BL92

5 Ndipo ananena kwa amuna a ku Sukoti, Mupatsetu anthu awa akunditsata mitanda yamkate; pakuti atopa, ndipo ndirikulondola Zeba ndi Tsalimuna mafumu a Midyani.

Werengani mutu wathunthu Oweruza 8

Onani Oweruza 8:5 nkhani