6 Koma akalonga a ku Sukoti anati, Kodi manja a Zeba ndi Tsalimuna ali m'dzanja lako tsopano apa, kuti ife tiwaninkhe ankhondo ako mkate?
Werengani mutu wathunthu Oweruza 8
Onani Oweruza 8:6 nkhani