Oweruza 8:7 BL92

7 Ndipo Gideoni anati, Cifukwa cace, Yehova akapereka Zeba ndi Tsalimuna m'dzanja langa, ndidzapuntha nyama yanu ndi minga ya m'cipululu ndi mitungwi.

Werengani mutu wathunthu Oweruza 8

Onani Oweruza 8:7 nkhani