Oweruza 9:26 BL92

26 Ndipo Gaala, mwana wa Ebedi anadza ndi abale ace, napita ku Sekemu; ndi eni ace a ku Sekemu anamkhulupirira.

Werengani mutu wathunthu Oweruza 9

Onani Oweruza 9:26 nkhani