Oweruza 9:27 BL92

27 Ndipo anaturuka kumka kuminda, nachera mphesa m'mindamo, naponda mphesa, napereka nsembe yolemekeza, nalowa m'nyumba ya mulungu wao, nadya, namwa, natemberera Abimeleki.

Werengani mutu wathunthu Oweruza 9

Onani Oweruza 9:27 nkhani