Oweruza 9:43 BL92

43 Pamenepo anatenga anthu, nawagawa magulu atatu, nalalira m'minda; napenya, ndipo taonani, anthu alimkuturuka m'mudzi; nawaukira iye nawakantha.

Werengani mutu wathunthu Oweruza 9

Onani Oweruza 9:43 nkhani