Oweruza 9:44 BL92

44 Ndi Abimeleki ndi magulu okhala naye anathamanga naima polowera pa cipata ca mudzi; ndi magulu awiriwo anagwera onse okhala m'munda, nawakantha.

Werengani mutu wathunthu Oweruza 9

Onani Oweruza 9:44 nkhani