1 Mafumu 1:15 BL92

15 Pamenepo Batiseba analowa kwa mfumu kucipinda; ndipo mfumuyo inali yokalamba ndithu; ndipo Abisagi wa ku Sunamu anali kutumikira mfumu.

Werengani mutu wathunthu 1 Mafumu 1

Onani 1 Mafumu 1:15 nkhani