1 Mafumu 1:21 BL92

21 Mukapanda kutero, kudzacitika, pamene mbuye wanga mfumu atagona kwa makolo ace, ine ndi mwana wanga Solomo tidzayesedwa ocimwa.

Werengani mutu wathunthu 1 Mafumu 1

Onani 1 Mafumu 1:21 nkhani