24 Ndipo Natani anati, Mbuye wanga mfumu, kodi inu munati, Adoniya adzakhala mfumu nditamuka ine, nadzakhala ndiye pa mpando wanga wacifumu?
Werengani mutu wathunthu 1 Mafumu 1
Onani 1 Mafumu 1:24 nkhani