1 Mafumu 1:27 BL92

27 Cinthu ici cacitika ndi mbuye wanga mfumu kodi, ndipo simunadziwitsa mnyamata wanu amene adzakhala pa mpando wacifumu wa mbuye wanga mfumu atamuka iye?

Werengani mutu wathunthu 1 Mafumu 1

Onani 1 Mafumu 1:27 nkhani