41 Ndipo Adoniya ndi oitanidwa onse anali ndi iye analimva atatha kudya. Ndipo Yoabu, pakumva kuomba kwa lipengalo, anati, Phokosolo ndi ciani kuti m'mudzi muli cibumo?
Werengani mutu wathunthu 1 Mafumu 1
Onani 1 Mafumu 1:41 nkhani