44 ndipo mfumu yatumanso Zadoki wansembe, ndi Natani mneneri, ndi Benaya mwana wa Yehoyada, ndi Akereti, ndi Apeleti aja, namkweza iye pa nyuru ya mfumu.
Werengani mutu wathunthu 1 Mafumu 1
Onani 1 Mafumu 1:44 nkhani