1 Mafumu 1:5 BL92

5 Pamenepo Adoniya mwana wa Hagiti anadzikuza, nati, Ndikhala mfumu ndine; nadzikonzera agareta ndi apakavalo ndi anthu makumi asanu omtsogolera mothamanga.

Werengani mutu wathunthu 1 Mafumu 1

Onani 1 Mafumu 1:5 nkhani