1 Mafumu 10:17 BL92

17 Ndi malihawo mazana atatu a golidi wonsansantha, libawo limodzi linapangidwa ndi miyeso itatu ya golidi; ndipo mfumu inazisungira zonse m'nyumba yochedwa Nkhalango ya Lebano.

Werengani mutu wathunthu 1 Mafumu 10

Onani 1 Mafumu 10:17 nkhani