1 Mafumu 10:26 BL92

26 Ndipo Solomo anasonkhanitsa, magareta ndi apakavalo; anali nao magareta cikwi cimodzi mphambu, mazana anai, ndi apakavalo zikwi khumi mphambu ziwiri, nawasungira m'midzi yosungamo magareta, ndi kwamfumu m'Yerusalemu.

Werengani mutu wathunthu 1 Mafumu 10

Onani 1 Mafumu 10:26 nkhani