1 Mafumu 11:11 BL92

11 Cifukwa cace Yehova ananena ndi Solomo, Popeza cinthu ici cacitika ndi iwe, ndipo sunasunga cipangano canga ndi malemba anga amene ndinakulamulira, zedi, ndidzakung'ambira ufumu ndi kuupatsa mnyamata wako.

Werengani mutu wathunthu 1 Mafumu 11

Onani 1 Mafumu 11:11 nkhani