1 Mafumu 11:23 BL92

23 Ndipo Mulungu anamuutsira mdani wina, ndiye Rezoni mwana wa Eliyada, amene adathawa mbuye wace Hadadezeri mfumu ya ku Zoba.

Werengani mutu wathunthu 1 Mafumu 11

Onani 1 Mafumu 11:23 nkhani