1 Mafumu 11:32 BL92

32 Koma iye adzakhala nalo pfuko limodzi, cifukwa ca Davide mtumiki wanga, ndi ca Yerusalemu, mudzi umene ndinausankha m'mafuko onse a Israyeli.

Werengani mutu wathunthu 1 Mafumu 11

Onani 1 Mafumu 11:32 nkhani