1 Mafumu 11:34 BL92

34 Koma sindidzalanda ufumu wonse m'dzanja lace, koma ndidzamkhalitsa mfumu masiku ace onse, cifukwa ca Davide mtumiki wanga amene uja ndinamsankha, cifukwa kuti anasunga malamulo anga ndi malemba anga.

Werengani mutu wathunthu 1 Mafumu 11

Onani 1 Mafumu 11:34 nkhani