1 Mafumu 11:36 BL92

36 Ndipo ndidzamninkha mwana wace pfuko limodzi, kuti Davide mtumiki wanga akhale cikhalire ndi nyali pamaso panga m'Yerusalemu, mudzi umene ndinadzisankhira kuikapo dzina langa.

Werengani mutu wathunthu 1 Mafumu 11

Onani 1 Mafumu 11:36 nkhani