15 Potero mfumu siinamvera anthuwo, pakuti kusintha uku kunacokera kwa Yehova, kuti akhazikitse mau ace amene Yehova ananenetsa Abiya wa ku Silo kwa Yerobiamu mwana wa Nebati.
Werengani mutu wathunthu 1 Mafumu 12
Onani 1 Mafumu 12:15 nkhani