1 Mafumu 12:2 BL92

2 Ndipo kunali kuti Yerobiamu mwana wa Nebati anacimva akali m'Aigupto, kumene anathawira kucokera ku maso a Solomo mfumu, pakuti Yerobiamu anakhala ku Aigupto.

Werengani mutu wathunthu 1 Mafumu 12

Onani 1 Mafumu 12:2 nkhani