1 Mafumu 12:20 BL92

20 Ndipo kunali, atamva Aisrayeli onse kuti Yerobiamu wabweranso, anatuma kumuitanira iye kumsonkhano, namlonga iye mfumu ya Aisrayeli onse; palibe munthu anatsata nyumba ya Davide koma pfuko lokha la Yuda.

Werengani mutu wathunthu 1 Mafumu 12

Onani 1 Mafumu 12:20 nkhani