14 Natsata munthu wa Mulungu, nampeza ali, tsonga patsinde pa mtengo wathundu, nanena naye, Kodi ndiwe munthu wa Mulungu amene uja anacokera ku Yuda? Nati, Ndine amene.
Werengani mutu wathunthu 1 Mafumu 13
Onani 1 Mafumu 13:14 nkhani