21 napfuula iye kwa munthu uja wa Mulungu anacokera ku Yudayo, nati, Atero Yehova, Pokhala sunamvera mau a pakamwa pa Yehova, osasunga lamulo lija Yehova Mulungu wako anakulamulira,
Werengani mutu wathunthu 1 Mafumu 13
Onani 1 Mafumu 13:21 nkhani