1 Mafumu 13:28 BL92

28 Namuka iye, napeza mtembo wace wogwera m'njira, ndi buru ndi mkango ziti ciimire pafupi ndi mtembo. Mkango udalibe kudya mtembo, kapena kukadzula buru.

Werengani mutu wathunthu 1 Mafumu 13

Onani 1 Mafumu 13:28 nkhani