3 Ndipo iye anapatsa cizindikilo tsiku lomwelo, nari, Cizindikilo cimene Yehova ananena ndi ici, Taonani guwali la nsembe lidzang'ambika, ndi phulusa liri pa ilo lidzatayika.
Werengani mutu wathunthu 1 Mafumu 13
Onani 1 Mafumu 13:3 nkhani