31 Ndipo kunacitika, atamuika iye, ananena ndi ana ace, nati, Nkadzamwalira ine mudzandiike ine m'manda momwemo mwaikidwa munthu wa Mulunguyo, ikani mafupa anga pafupi ndi mafupa ace.
Werengani mutu wathunthu 1 Mafumu 13
Onani 1 Mafumu 13:31 nkhani