33 Pambuyo pa ici Yerobiamu sanabwerera pa njira yace yoipa, koma analonganso anthu acabe akhale ansembe a misanje, yensewakufuna yemweyu anampatula akhale wansembe wa misanje,
Werengani mutu wathunthu 1 Mafumu 13
Onani 1 Mafumu 13:33 nkhani