9 Pakuti potero ndinalamulidwa ndi mau a Yehova, ndi kuti, Usakadye mkate, kapena kumwa madzi, kapena kubwerera njira yomweyo unadzerayo.
Werengani mutu wathunthu 1 Mafumu 13
Onani 1 Mafumu 13:9 nkhani