1 Mafumu 14:13 BL92

13 Ndipo Aisrayeli onse adzamlira, nadzamuika, popeza iye yekha wa ana a Yerobiamu adzalowa m'manda; pakuti mwa iye mwapezedwa cokoma ca kwa Yehova Mulungu wa Israyeli m'nyumba ya Yerobiamu.

Werengani mutu wathunthu 1 Mafumu 14

Onani 1 Mafumu 14:13 nkhani