1 Mafumu 14:17 BL92

17 Ndipo mkazi wa Yerobiamu ananyamuka nacoka, nafika ku Tiriza; ndipo polowa iye pa khomo la nyumba yace anatsirizika mwanayo.

Werengani mutu wathunthu 1 Mafumu 14

Onani 1 Mafumu 14:17 nkhani